Yobu 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho, ine sinditseka pakamwa panga.Ndilankhula chifukwa cha kuvutika mumtima,+Ndilankhula za nkhawa zanga, chifukwa moyo wanga ukupweteka. Yesaya 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi ndinene kuti chiyani? Kodi iyeyo andiuza kuti chiyani?+Iyeyonso wachitapo kanthu.+Zaka zanga zonse, ndikungokhalira kuyenda ndili khuma chifukwa cha chisoni cha mtima wanga.+
11 Choncho, ine sinditseka pakamwa panga.Ndilankhula chifukwa cha kuvutika mumtima,+Ndilankhula za nkhawa zanga, chifukwa moyo wanga ukupweteka.
15 Kodi ndinene kuti chiyani? Kodi iyeyo andiuza kuti chiyani?+Iyeyonso wachitapo kanthu.+Zaka zanga zonse, ndikungokhalira kuyenda ndili khuma chifukwa cha chisoni cha mtima wanga.+