Numeri 33:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Zikadzatero, zimene ndinafuna kuchita kwa anthuwo ndidzachita kwa inu.’”+ Deuteronomo 28:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+ Oweruza 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unayakira ana a Isiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Afilisiti+ ndi kwa ana a Amoni.+ Oweruza 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ana a Isiraeli anayambiranso kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ moti Yehova anawapereka m’manja mwa Afilisiti+ zaka 40.
48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+
7 Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unayakira ana a Isiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Afilisiti+ ndi kwa ana a Amoni.+
13 Tsopano ana a Isiraeli anayambiranso kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ moti Yehova anawapereka m’manja mwa Afilisiti+ zaka 40.