Genesis 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Potsirizira pake, Mulungu anakumbukira Rakele ndipo anamumvera n’kumuyankha mwa kum’patsa mphamvu zobereka.+
22 Potsirizira pake, Mulungu anakumbukira Rakele ndipo anamumvera n’kumuyankha mwa kum’patsa mphamvu zobereka.+