Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “‘Masiku onse a lonjezo lake lokhala Mnaziri, lezala lisadutse kumutu kwake+ kufikira atatha masiku ake amene anadzipereka kwa Yehova. Azikhala woyera mwa kusiya tsitsi+ lake la kumutu kuti likule.

  • Oweruza 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna. M’mutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri+ wa Mulungu potuluka m’mimba.+ Iye adzakhala patsogolo populumutsa Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+

  • Luka 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 chifukwa adzakhala wamkulu pamaso pa Yehova.+ Koma asadzamwe vinyo ngakhale pang’ono+ kapena chakumwa chaukali chilichonse. Ndipo adzadzazidwa ndi mzimu woyera kuyambira ali m’mimba mwa mayi ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena