Miyambo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu aliyense woyankhira nkhani asanaimvetsetse n’ngopusa,+ ndipo amachita manyazi.+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+