Oweruza 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero, iwo anayamba kuchotsa milungu yonse yachilendo pakati pawo+ n’kuyamba kutumikira Yehova,+ moti mtima wake+ unagwidwa ndi chisoni chifukwa cha kuvutika kwa ana a Isiraeli.+
16 Atatero, iwo anayamba kuchotsa milungu yonse yachilendo pakati pawo+ n’kuyamba kutumikira Yehova,+ moti mtima wake+ unagwidwa ndi chisoni chifukwa cha kuvutika kwa ana a Isiraeli.+