Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 18:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mizipe,+ Kefira,+ Moza,

  • Oweruza 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chotero ana onse a Isiraeli anatuluka,+ kuchokera ku Dani+ mpaka kumunsi ku Beere-seba,+ ndipo khamu lonselo linasonkhana pamodzi mogwirizana+ kwa Yehova ku Mizipa,+ pamodzinso ndi anthu a m’dera la Giliyadi.+

  • Oweruza 21:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano amuna a Isiraeli analumbira ali ku Mizipa+ kuti: “Aliyense wa ife sadzapereka mwana wake wamkazi kuti akwatiwe ndi mwamuna wa fuko la Benjamini.”+

  • 1 Samueli 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsopano Samueli anasonkhanitsa anthu onse pamodzi pamaso pa Yehova ku Mizipa+

  • 1 Mafumu 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno Mfumu Asa inaitanitsa Ayuda onse,+ moti palibe amene sanaitanidwe, ndipo iwo anatenga miyala ya ku Rama ndi matabwa ake, zimene Basa ankamangira. Mfumu Asa inatenga zinthu zimenezo n’kuyamba kukamangira mzinda wa Geba+ ku Benjamini, ndi mzinda wa Mizipa.+

  • 2 Mafumu 25:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Akuluakulu onse a magulu ankhondo+ ndi asilikali awo atamva kuti mfumu ya Babulo yasankha Gedaliya, nthawi yomweyo anapita kwa Gedaliya ku Mizipa.+ Akuluakuluwo anali Isimaeli mwana wa Netaniya, Yohanani mwana wa Kareya, Seraya mwana wa Tanumeti Mnetofa, ndi Yaazaniya mwana wa Amaakati, pamodzi ndi asilikali awo.

  • Yeremiya 40:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chotero Yeremiya anapita ku Mizipa+ kukakhala ndi Gedaliya+ mwana wa Ahikamu pakati pa anthu amene anatsala m’dzikolo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena