Yoswa 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anakafika ku Debiri kuchigwa cha Akori+ n’kukhotera kumpoto cha ku Giligala,+ patsogolo pa chitunda cha Adumi, kum’mwera kwa chigwa cha mtsinje. Malirewo anapitirira n’kukafika kumadzi a Eni-semesi,+ n’kukathera ku Eni-rogeli.+ 1 Samueli 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anthu onse anapita ku Giligala ndipo analonga Sauli kukhala mfumu pamaso pa Yehova ku Giligalako. Kenako anapereka nsembe zachiyanjano pamaso pa Yehova+ kumeneko, ndipo Sauli pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli anali osangalala kwambiri.+
7 Anakafika ku Debiri kuchigwa cha Akori+ n’kukhotera kumpoto cha ku Giligala,+ patsogolo pa chitunda cha Adumi, kum’mwera kwa chigwa cha mtsinje. Malirewo anapitirira n’kukafika kumadzi a Eni-semesi,+ n’kukathera ku Eni-rogeli.+
15 Choncho anthu onse anapita ku Giligala ndipo analonga Sauli kukhala mfumu pamaso pa Yehova ku Giligalako. Kenako anapereka nsembe zachiyanjano pamaso pa Yehova+ kumeneko, ndipo Sauli pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli anali osangalala kwambiri.+