Yobu 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Zikanakhala bwino masautso anga+ onse akanayezedwa kulemera kwake,Ndiponso pa nthawi yomweyo mavuto anga akanaikidwa pasikelo. Yobu 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Ineyo ndikunyansidwa ndi moyo wanga.+Ndilankhula mwamphamvu za nkhawa zanga.Ndilankhula chifukwa cha kuwawa kwa moyo wanga.
2 “Zikanakhala bwino masautso anga+ onse akanayezedwa kulemera kwake,Ndiponso pa nthawi yomweyo mavuto anga akanaikidwa pasikelo.
10 “Ineyo ndikunyansidwa ndi moyo wanga.+Ndilankhula mwamphamvu za nkhawa zanga.Ndilankhula chifukwa cha kuwawa kwa moyo wanga.