Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pamenepo wansembeyo anawauza kuti: “Pitani mu mtendere. Yehova ali ndi inu pa ulendowu.”

  • 1 Samueli 25:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Atatero, Davide analandira zimene Abigayeli anamubweretsera ndiyeno anamuuza kuti: “Pita kunyumba kwako mwamtendere.+ Taona, ndamvera mawu ako kuti ndichite zinthu mokuganizira.”+

  • Maliko 5:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Iye anauza mayiyo kuti: “Mwanawe, chikhulupiriro chako chakuchiritsa. Pita mu mtendere,+ matenda ako aakuluwo atheretu.”+

  • Luka 7:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Koma iye anauza mayiyo kuti: “Chikhulupiriro chako chakupulumutsa.+ Pita mu mtendere.”+

  • Luka 8:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Koma iye anauza mayiyo kuti: “Mwanawe, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.+ Pita mu mtendere.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena