Salimo 81:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu anga sanamvere mawu anga.+Ndipo Isiraeli sanasonyeze kuti ndi wofunitsitsa kundimvera.+ Yeremiya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano chifukwa chakuti mwapitiriza kuchita ntchito zimenezi,’ watero Yehova, ‘ndipo ndinali kukulankhulani nthawi zonse, kudzuka m’mamawa ndi kukulankhulani,+ koma inu osamva,+ kukuitanani koma inu osandiyankha,+ Ezekieli 33:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iwo adzabwera kwa iwe ngati mmene amachitira nthawi zonse ndipo adzakhala pamaso pako ngati anthu anga.+ Adzamva mawu ako koma sadzawatsatira,+ chifukwa ndi pakamwa pawo, akulankhula za zilakolako zawo zonyansa ndipo mtima wawo uli pa kupeza phindu mopanda chilungamo.+
11 Koma anthu anga sanamvere mawu anga.+Ndipo Isiraeli sanasonyeze kuti ndi wofunitsitsa kundimvera.+
13 Tsopano chifukwa chakuti mwapitiriza kuchita ntchito zimenezi,’ watero Yehova, ‘ndipo ndinali kukulankhulani nthawi zonse, kudzuka m’mamawa ndi kukulankhulani,+ koma inu osamva,+ kukuitanani koma inu osandiyankha,+
31 Iwo adzabwera kwa iwe ngati mmene amachitira nthawi zonse ndipo adzakhala pamaso pako ngati anthu anga.+ Adzamva mawu ako koma sadzawatsatira,+ chifukwa ndi pakamwa pawo, akulankhula za zilakolako zawo zonyansa ndipo mtima wawo uli pa kupeza phindu mopanda chilungamo.+