Genesis 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Sarai, mkazi wa Abulamu, sanamuberekere ana.+ Koma Saraiyo anali ndi kapolo wake Mwiguputo, dzina lake Hagara.+ Genesis 29:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yehova ataona kuti Leya sanali kukondedwa kwenikweni, anam’patsa mphamvu zobereka,+ koma Rakele anali wosabereka.+
16 Tsopano Sarai, mkazi wa Abulamu, sanamuberekere ana.+ Koma Saraiyo anali ndi kapolo wake Mwiguputo, dzina lake Hagara.+
31 Yehova ataona kuti Leya sanali kukondedwa kwenikweni, anam’patsa mphamvu zobereka,+ koma Rakele anali wosabereka.+