Genesis 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mwanayo anamutcha dzina lakuti Nowa,+ ndipo anati: “Uyu ndi amene adzatibweretsere mpumulo ku ntchito yathu yopweteketsa manja, chifukwa cholima nthaka imene Yehova anaitemberera.”+ Genesis 41:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Mwana woyambayo Yosefe anamutcha dzina lakuti Manase,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse, ndi nyumba yonse ya bambo anga.”+ Ekisodo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Patapita nthawi Zipora anabereka mwana wamwamuna ndipo Mose anati: “Dzina lake akhale Gerisomu,*+ chifukwa ndine mlendo m’dziko lino.”+ Mateyu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye adzabereka mwana wamwamuna, ndipo dzina lake udzamutche Yesu,*+ chifukwa adzapulumutsa+ anthu ake+ ku machimo awo.”+
29 Mwanayo anamutcha dzina lakuti Nowa,+ ndipo anati: “Uyu ndi amene adzatibweretsere mpumulo ku ntchito yathu yopweteketsa manja, chifukwa cholima nthaka imene Yehova anaitemberera.”+
51 Mwana woyambayo Yosefe anamutcha dzina lakuti Manase,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse, ndi nyumba yonse ya bambo anga.”+
22 Patapita nthawi Zipora anabereka mwana wamwamuna ndipo Mose anati: “Dzina lake akhale Gerisomu,*+ chifukwa ndine mlendo m’dziko lino.”+
21 Iye adzabereka mwana wamwamuna, ndipo dzina lake udzamutche Yesu,*+ chifukwa adzapulumutsa+ anthu ake+ ku machimo awo.”+