Mateyu 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna, ndipo mudzapeza. Gogodanibe,+ ndipo adzakutsegulirani. 1 Yohane 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+
7 “Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna, ndipo mudzapeza. Gogodanibe,+ ndipo adzakutsegulirani.
14 Ifetu timamudalira+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi chifuniro chake, amatimvera.+