1 Samueli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika kumeneko anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba, koma ana ako sakutsatira chitsanzo chako. Ndiye tikufuna kuti utiikire mfumu+ yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.” 1 Samueli 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Samueli anamvera mawu onse amene anthuwo ananena, kenako anafotokozera Yehova mawuwo.+
5 Atafika kumeneko anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba, koma ana ako sakutsatira chitsanzo chako. Ndiye tikufuna kuti utiikire mfumu+ yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.”