Numeri 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiponso muzikapereka vinyo monga nsembe yachakumwa.+ Vinyoyo azikakhala wokwanira hafu ya muyezo wa hini. Akakhale nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.
10 Ndiponso muzikapereka vinyo monga nsembe yachakumwa.+ Vinyoyo azikakhala wokwanira hafu ya muyezo wa hini. Akakhale nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.