1 Samueli 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Poyankha, Yehova anauza Samueli+ kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akunena kwa iwe,+ pakuti sanakane iweyo koma akana ine kuti ndisakhale mfumu yawo.+ Hoseya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndinakupatsa mfumu nditakwiya+ ndipo ndidzaichotsa nditakwiya.+
7 Poyankha, Yehova anauza Samueli+ kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akunena kwa iwe,+ pakuti sanakane iweyo koma akana ine kuti ndisakhale mfumu yawo.+