Salimo 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Bwerani kuno ana anga, ndimvetsereni.+Ndikuphunzitsani kuopa Yehova.+ Miyambo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzakutsogolera m’njira ya nzeru.+ Ndidzakuchititsa kuyenda m’njira zowongoka.+