1 Samueli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho utsogole kupita ku Giligala.+ Inenso ndipita kumeneko kuti ndikapereke nsembe zopsereza ndi kupereka nsembe zachiyanjano.+ Ukandidikire masiku 7+ mpaka nditakupeza, ndipo ndikadzafika ndidzakuuza zoti uchite.” Yeremiya 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+ Yeremiya 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inetu ndinalangiza makolo anu pamene ndinali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo+ ndipo ndikupitiriza kutero. Ndinali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwalangiza kuti: “Muzimvera mawu anga.”+
8 Choncho utsogole kupita ku Giligala.+ Inenso ndipita kumeneko kuti ndikapereke nsembe zopsereza ndi kupereka nsembe zachiyanjano.+ Ukandidikire masiku 7+ mpaka nditakupeza, ndipo ndikadzafika ndidzakuuza zoti uchite.”
23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+
7 Inetu ndinalangiza makolo anu pamene ndinali kuwatulutsa m’dziko la Iguputo+ ndipo ndikupitiriza kutero. Ndinali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwalangiza kuti: “Muzimvera mawu anga.”+