Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Anthu amene uli nawowa ndi ochuluka kwambiri kuti ndipereke Amidiyani m’manja mwawo,+ chifukwa mwina Isiraeli angadzitukumule+ pamaso panga ndi kunena kuti, ‘Ndinadzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.’+

  • 2 Mafumu 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma iye anati: “Usaope,+ popeza ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi iwowo.”+

  • 2 Mbiri 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano Asa anayamba kupemphera kwa Yehova Mulungu wake,+ kuti: “Inu Yehova mukafuna kuthandiza, zilibe kanthu kuti anthuwo ndi ambiri kapena ndi opanda mphamvu.+ Tithandizeni Yehova Mulungu wathu chifukwa tikudalira inu,+ ndipo tabwera m’dzina lanu+ kudzamenyana ndi khamuli. Inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+ Musalole kuti munthu akuposeni mphamvu.”+

  • Salimo 115:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu oopa Yehova, khulupirirani Yehova.+

      Iye ndiye thandizo lanu ndi chishango chanu.+

  • Aheberi 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Mwa chikhulupiriro, anthu amenewa anagonjetsa maufumu pa nkhondo,+ anachita chilungamo,+ analandira malonjezo+ ndiponso anatseka mikango pakamwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena