1 Samueli 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma akatiuza kuti, ‘Bwerani kuno mudzamenyane nafe!’ ife tipita chifukwa Yehova adzawaperekadi m’manja mwathu, ndipo chimenechi ndicho chizindikiro chathu.”+ 1 Samueli 17:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Tangoyerekeza kubwera kuno, ndipereka mnofu wako kwa mbalame zam’mlengalenga ndi kwa zilombo zakutchire.”+ 2 Mafumu 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Amaziya anatumiza amithenga kwa Yehoasi mwana wa Yehoahazi mwana wa Yehu mfumu ya Isiraeli, ndi uthenga wakuti: “Bwera tidzamenyane.”+
10 Koma akatiuza kuti, ‘Bwerani kuno mudzamenyane nafe!’ ife tipita chifukwa Yehova adzawaperekadi m’manja mwathu, ndipo chimenechi ndicho chizindikiro chathu.”+
44 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Tangoyerekeza kubwera kuno, ndipereka mnofu wako kwa mbalame zam’mlengalenga ndi kwa zilombo zakutchire.”+
8 Tsopano Amaziya anatumiza amithenga kwa Yehoasi mwana wa Yehoahazi mwana wa Yehu mfumu ya Isiraeli, ndi uthenga wakuti: “Bwera tidzamenyane.”+