1 Samueli 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+ 1 Samueli 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyi Sauli anali kukhala kunja kwa mzinda wa Gibeya+ pansi pa mtengo wa makangaza* umene uli ku Migironi. Iye anali ndi amuna pafupifupi 600.+
26 Koma Sauli anapita kwawo ku Gibeya,+ ndipo amuna olimba mtima amene Mulungu anakhudza mitima yawo anapita naye pamodzi.+
2 Pa nthawiyi Sauli anali kukhala kunja kwa mzinda wa Gibeya+ pansi pa mtengo wa makangaza* umene uli ku Migironi. Iye anali ndi amuna pafupifupi 600.+