1 Samueli 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anamupatsanso chidutswa cha nkhuyu zouma zoumba pamodzi ndi zidutswa ziwiri za mphesa zouma zoumba pamodzi.+ Iye anadya ndipo anapezanso mphamvu,+ chifukwa sanadye mkate kapena kumwa madzi kwa masiku atatu, usana ndi usiku.
12 Anamupatsanso chidutswa cha nkhuyu zouma zoumba pamodzi ndi zidutswa ziwiri za mphesa zouma zoumba pamodzi.+ Iye anadya ndipo anapezanso mphamvu,+ chifukwa sanadye mkate kapena kumwa madzi kwa masiku atatu, usana ndi usiku.