2 Samueli 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo atumiki a mfumu anauza mfumu kuti: “Ife atumiki anu tichita mogwirizana ndi zimene inu mbuyathu mfumu mwasankha.”+ Mlaliki 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa mawu a mfumu ali ndi mphamvu yolamulira,+ ndipo ndani angaifunse kuti: ‘Kodi mukuchita chiyani?’”
15 Pamenepo atumiki a mfumu anauza mfumu kuti: “Ife atumiki anu tichita mogwirizana ndi zimene inu mbuyathu mfumu mwasankha.”+
4 chifukwa mawu a mfumu ali ndi mphamvu yolamulira,+ ndipo ndani angaifunse kuti: ‘Kodi mukuchita chiyani?’”