-
Yoswa 7:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndiyeno Yoswa anadzuka m’mawa kwambiri, n’kuuza Isiraeli kuti afike pamaso pa Mulungu, fuko ndi fuko, ndipo fuko la Yuda linasankhidwa.
-