Deuteronomo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndipo uyandikire pafupi ndi ana a Amoni. Usawavutitse kapena kumenyana nawo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko la ana a Amoni kuti likhale lako. Dziko limeneli ndinalipereka kwa ana a Loti kuti likhale lawo.+ 1 Samueli 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsiku lotsatira, Sauli+ anagawa anthuwo m’magulu atatu.+ Amenewa analowa pakati pa msasawo pa ulonda wa m’mawa.*+ Atatero, anayamba kukantha Aamoni+ kufikira dzuwa litatentha. Otsala anawabalalitsa moti sipanatsale anthu awiri ali limodzi.+
19 ndipo uyandikire pafupi ndi ana a Amoni. Usawavutitse kapena kumenyana nawo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko la ana a Amoni kuti likhale lako. Dziko limeneli ndinalipereka kwa ana a Loti kuti likhale lawo.+
11 Tsiku lotsatira, Sauli+ anagawa anthuwo m’magulu atatu.+ Amenewa analowa pakati pa msasawo pa ulonda wa m’mawa.*+ Atatero, anayamba kukantha Aamoni+ kufikira dzuwa litatentha. Otsala anawabalalitsa moti sipanatsale anthu awiri ali limodzi.+