Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 36:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chotero Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Esau analinso kutchedwa Edomu.+

  • Genesis 36:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 mfumu Magidieli ndi mfumu Iramu. Amenewa ndiwo anali mafumu a Edomu+ monga mwa madera awo m’dziko lawo.+ Iyi ndiyo mibadwo ya Esau, kholo la Aedomu.+

  • Malaki 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Popeza kuti Edomu akunena kuti, ‘Ife tawonongedwa, koma tibwerera ndi kukamanga malo athu owonongedwawo,’ Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Iwo akamanga, koma ine ndikagwetsa.+ Anthu adzatcha malo awowo, “dera la zoipa” ndipo iwowo adzatchedwa, “anthu okanidwa ndi Yehova+ mpaka kalekale.”*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena