Luka 1:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Wakhutitsa anthu anjala ndi zinthu zabwino,+ amene anali ndi chuma wawapitikitsa chimanjamanja.+