Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndipo kanthu kalikonse koyenera kuwonongedwa* kasamamatire kudzanja lanu,+ kuti mkwiyo woyaka moto wa Yehova usiye kukuyakirani+ ndipo akuchitireni chifundo ndi kukumverani chisoni,+ kutinso akuchulukitseni, monga mmene analumbirira makolo anu.+

  • 1 Samueli 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma Sauli ndi anthu ake anamvera chisoni Agagi ndipo sanaphe nkhosa ndi ng’ombe zabwino kwambiri,+ ziweto zonenepa, nkhosa zamphongo ndi zina zonse zimene zinali zabwino. Iwo sanafune kupha zimenezi,+ koma anawononga zinthu zina zonse zimene zinali zonyansa ndi zonyozeka.

  • Miyambo 28:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+

  • Aefeso 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti mfundo iyi mukuidziwa, ndipo mukuimvetsa bwino, kuti wadama+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndiwo kupembedza mafano, sadzalowa mu ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena