Miyambo 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu woipa amakhala ndi nkhope yamwano,+ koma wowongoka mtima ndi amene njira zake zidzakhazikike.+ Miyambo 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Wodala ndi munthu amene amaopa Mulungu nthawi zonse,+ koma woumitsa mtima wake adzagwera m’tsoka.+
29 Munthu woipa amakhala ndi nkhope yamwano,+ koma wowongoka mtima ndi amene njira zake zidzakhazikike.+
14 Wodala ndi munthu amene amaopa Mulungu nthawi zonse,+ koma woumitsa mtima wake adzagwera m’tsoka.+