Yeremiya 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+ Yeremiya 38:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yeremiya anati: “Sadzakuperekani m’manja mwawo mwa njira imeneyo. Chonde, mverani mawu a Yehova amene ndikukuuzani. Mukatero, zinthu zidzakuyenderani bwino+ ndipo mudzakhalabe ndi moyo.
23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+
20 Koma Yeremiya anati: “Sadzakuperekani m’manja mwawo mwa njira imeneyo. Chonde, mverani mawu a Yehova amene ndikukuuzani. Mukatero, zinthu zidzakuyenderani bwino+ ndipo mudzakhalabe ndi moyo.