Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye anawauza kuti: “Izi ndi zimene mfumu yokulamuliraniyo izidzafuna kwa inu:+ Idzatenga ana anu+ kuti azikayenda m’magaleta*+ ake ndi kukwera pamahatchi*+ ake, ndipo ena mwa ana anuwo azidzathamanga patsogolo pa magaleta ake.+

  • 1 Samueli 16:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Zitatero, Sauli anatumiza uthenga kwa Jese, kuti: “Chonde, lola kuti Davide apitirize kunditumikira, chifukwa ndam’konda.”

  • 1 Samueli 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Davide anali kupita kwa Sauli ndi kubwerera ku Betelehemu kukaweta nkhosa+ za bambo ake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena