Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 29:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo akalonga a Afilisiti anam’psera mtima kwambiri Akisi, ndipo anati: “Muuze abwerere,+ apite kumalo amene unam’patsa. Usamulole kuti apite nafe kunkhondo chifukwa angakatitembenukire+ kumeneko. Ukuganiza kuti munthu ameneyu adzakometsera dzina lake ndi chiyani kwa mbuye wake? Si mitu ya asilikali athu kodi?

  • 1 Mafumu 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tsopano Yehova Mulungu wanga wandipatsa mpumulo pakati pa adani anga onse ondizungulira.+ Palibe amene akulimbana nane, ndipo palibe choipa chilichonse chimene chikuchitika.+

  • Mateyu 16:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma iye anatembenuka n’kuuza Petulo kuti: “Pita kumbuyo kwanga, Satana!+ Ndiwe chopunthwitsa kwa ine, chifukwa zimene umaganiza si maganizo a Mulungu,+ koma maganizo a anthu.”

  • Yakobo 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 chifukwa mkwiyo wa munthu subala chilungamo cha Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena