2 Samueli 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno mfumu inaitana Ziba, mtumiki wa Sauli, ndi kumuuza kuti: “Chilichonse chimene chinali cha Sauli komanso chilichonse cha m’nyumba yake yonse, ine ndikupereka+ kwa mdzukulu wa mbuye wako.
9 Ndiyeno mfumu inaitana Ziba, mtumiki wa Sauli, ndi kumuuza kuti: “Chilichonse chimene chinali cha Sauli komanso chilichonse cha m’nyumba yake yonse, ine ndikupereka+ kwa mdzukulu wa mbuye wako.