Mateyu 5:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ngati munthu akufuna kukutengera kukhoti kuti akulande malaya ako amkati, m’patsenso akunja.+ 1 Akorinto 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kunena zoona, ndiye kuti mwalephereratu ngati mukutengerana kukhoti.+ Bwanji osangolola kulakwiridwa?+ Bwanji osalola kuberedwa?+
7 Kunena zoona, ndiye kuti mwalephereratu ngati mukutengerana kukhoti.+ Bwanji osangolola kulakwiridwa?+ Bwanji osalola kuberedwa?+