Genesis 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yakobo atangowaona, anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!”+ Chotero malowo anawatcha kuti Mahanaimu.*+ Yoswa 21:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kuchokera m’fuko la Gadi,+ anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake, wa Ramoti ku Giliyadi,+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Anawapatsanso Mahanaimu+ ndi malo ake odyetserako ziweto, 2 Samueli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+ 2 Samueli 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Davide anafika ku Mahanaimu+ ndipo Abisalomu nayenso anawoloka Yorodano pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli amene anali naye.
2 Yakobo atangowaona, anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!”+ Chotero malowo anawatcha kuti Mahanaimu.*+
38 Kuchokera m’fuko la Gadi,+ anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake, wa Ramoti ku Giliyadi,+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Anawapatsanso Mahanaimu+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+
24 Davide anafika ku Mahanaimu+ ndipo Abisalomu nayenso anawoloka Yorodano pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli amene anali naye.