Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 47:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndikufuna ndikagone limodzi ndi makolo anga.+ Choncho udzandinyamule ku Iguputo kuno, ukandiike m’manda a makolo anga.”+ Yosefe anayankha kuti: “Ndidzachitadi monga mwa mawu anu.”

  • Genesis 49:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Atatero anawalamula kuti: “Ine uno ndi ulendo wopita kumene kunapita makolo anga.+ Mukandiike limodzi ndi makolo anga, m’phanga limene lili m’munda wa Efuroni, Mhiti.+

  • Genesis 50:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anamunyamula n’kupita naye kudziko la Kanani. Kumeneko anakamuika m’phanga m’munda wa Makipela, woyang’anana ndi munda wa Mamure.+ Mundawo ndi umene Abulahamu anagula kwa Efuroni Mhiti, kuti akhale ndi manda.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena