2 Samueli 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo Abineri anayamba kufuulira Yowabu kuti: “Kodi tipitiriza kuphana ndi lupanga mpaka liti?+ Kodi sukudziwa kuti mapeto ake zimenezi zibweretsa mavuto aakulu?+ Kodi uwauza liti anthuwa kuti atembenuke ndi kusiya kutsatira abale awo?”+
26 Pamenepo Abineri anayamba kufuulira Yowabu kuti: “Kodi tipitiriza kuphana ndi lupanga mpaka liti?+ Kodi sukudziwa kuti mapeto ake zimenezi zibweretsa mavuto aakulu?+ Kodi uwauza liti anthuwa kuti atembenuke ndi kusiya kutsatira abale awo?”+