1 Mafumu 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ana a Barizilai+ Mgiliyadi uwasonyeze kukoma mtima kosatha. Azikhala pakati pa anthu odyera nawe limodzi patebulo,+ chifukwa anandithandiza+ pa nthawi imene ndinali kuthawa m’bale wako Abisalomu.+
7 “Ana a Barizilai+ Mgiliyadi uwasonyeze kukoma mtima kosatha. Azikhala pakati pa anthu odyera nawe limodzi patebulo,+ chifukwa anandithandiza+ pa nthawi imene ndinali kuthawa m’bale wako Abisalomu.+