2 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno pambuyo pake, Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndipite ku umodzi mwa mizinda ya Yuda?” Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+ 2 Samueli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anapitanso ndi amuna+ amene anali kuyenda naye, aliyense ndi banja lake. Iwo anakakhala m’mizinda ya m’dera la Heburoni. 1 Mbiri 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Patapita nthawi, Aisiraeli+ onse anasonkhana kwa Davide ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+
2 Ndiyeno pambuyo pake, Davide anayamba kufunsira kwa Yehova,+ kuti: “Kodi ndipite ku umodzi mwa mizinda ya Yuda?” Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Pita.” Davide anafunsanso kuti: “Ndipite kuti?” Iye anamuyankha kuti: “Ku Heburoni.”+
3 Davide anapitanso ndi amuna+ amene anali kuyenda naye, aliyense ndi banja lake. Iwo anakakhala m’mizinda ya m’dera la Heburoni.
11 Patapita nthawi, Aisiraeli+ onse anasonkhana kwa Davide ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+