2 Samueli 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine ndikuimira anthu ofuna mtendere+ ndi okhulupirika+ a mu Isiraeli. Iwe ukufuna kupha mzinda+ ndi mayi mu Isiraeli. N’chifukwa chiyani ukufuna kuwononga+ cholowa+ cha Yehova?”
19 Ine ndikuimira anthu ofuna mtendere+ ndi okhulupirika+ a mu Isiraeli. Iwe ukufuna kupha mzinda+ ndi mayi mu Isiraeli. N’chifukwa chiyani ukufuna kuwononga+ cholowa+ cha Yehova?”