1 Samueli 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli anali kukonda Davide, ndipo anthu anauza Sauli zimenezi. Sauli atamva nkhani imeneyi anasangalala. 1 Samueli 25:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma Sauli anali atapereka Mikala+ mwana wake wamkazi, mkazi wake wa Davide, kwa Paliti,+ mwana wamwamuna wa Laisi wa ku Galimu.+ 2 Samueli 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anatumizanso mithenga kwa Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi uthenga wonena kuti: “Ndipatse mkazi wanga Mikala, amene ndinalonjeza kumukwatira mwa kupereka makungu 100 akunsonga+ a Afilisiti.” 2 Samueli 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli sanakhalepo ndi mwana mpaka tsiku la imfa yake.
20 Tsopano Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli anali kukonda Davide, ndipo anthu anauza Sauli zimenezi. Sauli atamva nkhani imeneyi anasangalala.
44 Koma Sauli anali atapereka Mikala+ mwana wake wamkazi, mkazi wake wa Davide, kwa Paliti,+ mwana wamwamuna wa Laisi wa ku Galimu.+
14 Davide anatumizanso mithenga kwa Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi uthenga wonena kuti: “Ndipatse mkazi wanga Mikala, amene ndinalonjeza kumukwatira mwa kupereka makungu 100 akunsonga+ a Afilisiti.”