Numeri 35:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndipo musalandire dipo lowombolera moyo wa munthu wakupha mnzake, chifukwa ndi woyenera kuphedwa.+ Aphedwe ndithu ameneyo.+ Deuteronomo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Diso lako lisamumvere chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.+ 1 Samueli 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Samueli anati: “Monga mmene akazi anaferedwera ana awo chifukwa cha lupanga lako,+ momwemonso mayi ako+ aferedwa ana koposa akazi onse.”+ Pamenepo Samueli anadula Agagi nthulinthuli pamaso pa Yehova ku Giligala.+
31 Ndipo musalandire dipo lowombolera moyo wa munthu wakupha mnzake, chifukwa ndi woyenera kuphedwa.+ Aphedwe ndithu ameneyo.+
21 Diso lako lisamumvere chisoni.+ Pazikhala moyo kulipira moyo, diso kulipira diso, dzino kulipira dzino, dzanja kulipira dzanja, phazi kulipira phazi.+
33 Koma Samueli anati: “Monga mmene akazi anaferedwera ana awo chifukwa cha lupanga lako,+ momwemonso mayi ako+ aferedwa ana koposa akazi onse.”+ Pamenepo Samueli anadula Agagi nthulinthuli pamaso pa Yehova ku Giligala.+