Rute 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Boazi anamuyankha kuti: “Ndamva zonse zimene wachitira apongozi ako chimwalilireni mwamuna wako.+ Ndamvanso kuti unasiya bambo ako ndi mayi ako, komanso dziko la abale ako, n’kubwera kuno kwa anthu amene sunali kuwadziwa n’kale lonse.+
11 Ndiyeno Boazi anamuyankha kuti: “Ndamva zonse zimene wachitira apongozi ako chimwalilireni mwamuna wako.+ Ndamvanso kuti unasiya bambo ako ndi mayi ako, komanso dziko la abale ako, n’kubwera kuno kwa anthu amene sunali kuwadziwa n’kale lonse.+