Genesis 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano nayi mbiri ya Nowa. Nowa anali munthu wolungama.+ Iye anali wopanda cholakwa pakati pa anthu a m’nthawi yake. Nowa anayenda ndi Mulungu woona.+ Genesis 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+ Deuteronomo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ukhale wopanda cholakwa pamaso pa Yehova Mulungu wako.+ Salimo 84:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+
9 Tsopano nayi mbiri ya Nowa. Nowa anali munthu wolungama.+ Iye anali wopanda cholakwa pakati pa anthu a m’nthawi yake. Nowa anayenda ndi Mulungu woona.+
17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+
11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+