Yobu 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti iye amapereka mphoto kwa munthu wochokera kufumbi malinga ndi zochita zake,+Ndipo amam’bweretsera zinthu zogwirizana ndi njira yake. Salimo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+ Yesaya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+ Aheberi 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiponso, popanda chikhulupiriro+ n’zosatheka kukondweretsa Mulungu.+ Pakuti aliyense wofika kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti iye alikodi,+ ndi kuti amapereka mphoto+ kwa anthu omufunafuna ndi mtima wonse.+
11 Pakuti iye amapereka mphoto kwa munthu wochokera kufumbi malinga ndi zochita zake,+Ndipo amam’bweretsera zinthu zogwirizana ndi njira yake.
8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+
10 Amuna inu, nenani kuti anthu olungama zidzawayendera bwino,+ chifukwa adzadya zipatso za zochita zawo.+
6 Ndiponso, popanda chikhulupiriro+ n’zosatheka kukondweretsa Mulungu.+ Pakuti aliyense wofika kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti iye alikodi,+ ndi kuti amapereka mphoto+ kwa anthu omufunafuna ndi mtima wonse.+