Deuteronomo 28:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ngakhale kuti mwachuluka ngati nyenyezi zakumwamba,+ mudzatsala ochepa+ chifukwa chosamvera mawu a Yehova Mulungu wanu. Salimo 125:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma anthu obwerera kunjira zawo zokhotakhota,+Yehova adzawapereka ku chilango pamodzi ndi ochita zopweteka anzawo.+Ndipo mu Isiraeli mudzakhala mtendere.+ Aroma 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+
62 Ngakhale kuti mwachuluka ngati nyenyezi zakumwamba,+ mudzatsala ochepa+ chifukwa chosamvera mawu a Yehova Mulungu wanu.
5 Koma anthu obwerera kunjira zawo zokhotakhota,+Yehova adzawapereka ku chilango pamodzi ndi ochita zopweteka anzawo.+Ndipo mu Isiraeli mudzakhala mtendere.+
28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+