Salimo 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapazi anga ayendebe m’njira zanu,+Mmene sadzapunthwa ngakhale pang’ono.+