1 Samueli 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero Davide anapita ku Keila ndi amuna amene anali kuyenda naye, kukamenyana ndi Afilisitiwo. Iye anawalanda ziweto zawo ndipo anapha Afilisiti ochuluka kwambiri, moti Davide anakhala mpulumutsi wa anthu a mumzinda wa Keila.+ Salimo 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munakondwera nawo.+
5 Chotero Davide anapita ku Keila ndi amuna amene anali kuyenda naye, kukamenyana ndi Afilisitiwo. Iye anawalanda ziweto zawo ndipo anapha Afilisiti ochuluka kwambiri, moti Davide anakhala mpulumutsi wa anthu a mumzinda wa Keila.+
3 Pakuti iwo sanatenge dzikolo chifukwa cha lupanga lawo,+Ndipo si mkono wawo umene unawabweretsera chipulumutso.+Koma chinabwera ndi dzanja lanu lamanja,+ mkono wanu ndi kuwala kwa nkhope yanu,Chifukwa munakondwera nawo.+