Levitiko 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno ana ake anam’bweretsera magazi+ a ng’ombeyo, ndipo iye anaviika chala chake m’magaziwo+ ndi kuwapaka panyanga za guwa lansembe.+ Magazi otsala anawathira pansi pa guwa lansembelo. Levitiko 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu akapita kosaka nyama, ndipo wapha nyama kapena mbalame yololeka kudya, azithira magazi ake pansi+ ndi kuwafotsera ndi dothi.+
9 Ndiyeno ana ake anam’bweretsera magazi+ a ng’ombeyo, ndipo iye anaviika chala chake m’magaziwo+ ndi kuwapaka panyanga za guwa lansembe.+ Magazi otsala anawathira pansi pa guwa lansembelo.
13 “‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu akapita kosaka nyama, ndipo wapha nyama kapena mbalame yololeka kudya, azithira magazi ake pansi+ ndi kuwafotsera ndi dothi.+